Kukwanilitsa
Zolondola Komaso Kupereka Thandizo
ku Malawi ndi Rwanda.
Mrili wa COVID-19 wasokoneza miyoyo komaso makhalidwe amabanja pa dziko lonse la pansi. Malawi ndi Rwanda ndimayiko osapanga bwino pa khani zachuma anatenga njira zosiyanilanako ndi ena pothana ndi mriliyu mu chaka cha 2020, mriliyu wakhuza anthu akumudzi pa moyo wawo ya tsiku ndi tsiku ndi kapezedwe kawo kandalama (chuma) komaso kulimbana ndi kusitha kwa nyengo.
CCC19 Project Introduction
Zolinga za Ntchito ya CCC19
1Kupanga kafukufuku ndi mabungwe kuti timvetsetse kulumikizana pakati pa COVID-19 ndi kulimbana ndi kusitha kwa nyengo.
2kupeza nzeru zatsopano pa kugwirizana pakati pa COVID-19 ndi kusitha kwa nyengo pokhozekera kulimbana ndi kusitha kwa nyengo kwa mtsogolo chifukwa cha COVI-19
3Kupanga ndi kuyelekeza mauthenga ogwirizana potengera zaumoyo ndi kusitha kwa nyengo kwa anthu osalidwa ku Malawi ndi ku Rwanda kuzera munjira zosiyana siyana pakati pa amayi komaso abambo
4Kutulutsa zinthokozo kuzera munjira zoyenera zosiyana siyana kwa magulu okhuzidwa ku Malawi, Rwanda ndi UK
Zofanana koma
zosiyanasiyana
A CCC19 amalemekeza kusiyana pakati pa amayi ndi abambo, zaka, mutundu, chipembezo komaso ulumali ndipo ndiwofunisitsa kupanga izi munjila ina iliyose.Timaziwa kuti kafukufuku woti aliyetse watengapo gawo umakhala ndi zosatila za bwino. kuti tipereke ukadaulo wodalilika ndi kupitisa pasogolo chithandizo ku Malawi ndi Rwanda, tinasonkhezera zoyerekeza...
Dr. Laine Munir
Center of Excellence in Biodiversity and Natural Resource Management,
University of Rwanda (UR)
Abwezi










Osogolera Ntchito

Dr. Michael Mikulewicz
Wofufuza Wamkulu

Prof. Beth Kaplin
Othandizila Kafukufuku ku Rwanda

Dr. Griphin Chirambo
Othandizila Kafukufuku ku Malawi